-
Yesaya 6:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Aliyense ankauza mnzake kuti:
“Woyera, woyera, woyera ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+
Dziko lonse lapansi ladzaza ndi ulemerero wake.”
-