Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 34:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kodi ndi ndani pakati panu amene amakonda moyo,

      Ndipo angakonde atakhala ndi moyo wabwino kwa masiku ambiri?+

      נ [Nun]

      13 Ndiyetu muteteze lilime lanu ku zinthu zoipa,+

      Komanso milomo yanu kuti isalankhule chinyengo.+

  • Malaki 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndidzakuyandikirani kuti ndikuweruzeni. Sindidzazengereza kupereka umboni wotsutsa amatsenga,+ achigololo, olumbira monama+ komanso amene amachitira zachinyengo munthu waganyu,+ mkazi wamasiye ndi mwana wamasiye*+ komanso amene amakana kuthandiza alendo.+ Anthu amenewa sakundiopa,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani