-
Salimo 143:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Inu Yehova, ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo chifukwa cha dzina lanu.
Ndipulumutseni mʼmavuto anga, chifukwa ndinu wachilungamo.+
-
-
Ezekieli 36:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 “Choncho uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Sindidzachita zimenezi chifukwa cha inuyo a nyumba ya Isiraeli, koma chifukwa cha dzina langa loyera limene munalidetsa pakati pa anthu a mitundu ina kumene munapita.”’+
-