2 Samueli 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwina Yehova aona mavuto anga,+ ndipo Yehova adzabwezeretsa zabwino kwa ine mʼmalo mwa zimene Simeyi akunena lero pondinyoza.”+
12 Mwina Yehova aona mavuto anga,+ ndipo Yehova adzabwezeretsa zabwino kwa ine mʼmalo mwa zimene Simeyi akunena lero pondinyoza.”+