-
1 Samueli 25:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Munthu akakuukirani ndi kufunafuna moyo wanu, Yehova Mulungu wanu adzakulunga moyo wanu mʼphukusi la moyo kuti utetezeke. Koma moyo wa adani anu adzauponya kutali ngati mmene munthu amaponyera mwala ndi gulaye.*
-