-
2 Mbiri 20:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Choncho Yahazieli anati: “Tamverani Ayuda nonsenu, anthu a ku Yerusalemu ndi inu Mfumu Yehosafati! Yehova akukuuzani kuti, ‘Musaope kapena kuchita mantha ndi gulu lalikululi chifukwa nkhondoyi si yanu, ndi ya Mulungu.+
-