-
Salimo 59:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Chifukwa cha tchimo lapakamwa pawo ndi mawu a milomo yawo,
Ndiponso chifukwa cha mawu otukwana komanso achinyengo amene amalankhula,+
Akodwe ndi kunyada kwawoko.
-
-
Yeremiya 18:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Mʼnyumba zawo mumveke kulira
Mukawabweretsera magulu achifwamba mwadzidzidzi.
Chifukwa akumba dzenje kuti andigwire
Ndipo atchera misampha kuti akole mapazi anga.+
-