Salimo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa simudzandisiya* mʼManda.*+ Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.*+ Salimo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndikuitana inu Yehova, Thanthwe langa,+Musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana. Mukakhala chete pamene ndikukuitanani,Ndidzafanana ndi anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+ Yesaya 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mʼmalo mopeza mtendere ndinali ndi chisoni chachikulu.Koma chifukwa chakuti mumandikonda kwambiri,Munanditeteza kuti ndisapite kudzenje lachiwonongeko.+ Machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.*+ Yona 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
28 Ndikuitana inu Yehova, Thanthwe langa,+Musatseke makutu anu pamene ine ndikuitana. Mukakhala chete pamene ndikukuitanani,Ndidzafanana ndi anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+
17 Mʼmalo mopeza mtendere ndinali ndi chisoni chachikulu.Koma chifukwa chakuti mumandikonda kwambiri,Munanditeteza kuti ndisapite kudzenje lachiwonongeko.+ Machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.*+