2 Samueli 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Davide anauzidwa kuti: “Ahitofeli nayenso ali mʼgulu la anthu amene akukonza chiwembu+ ndi Abisalomu.”+ Davide atamva zimenezi anati: “Chonde Yehova,+ chititsani kuti malangizo a Ahitofeli akhale opusa.”+ 2 Samueli 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 7:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
31 Kenako Davide anauzidwa kuti: “Ahitofeli nayenso ali mʼgulu la anthu amene akukonza chiwembu+ ndi Abisalomu.”+ Davide atamva zimenezi anati: “Chonde Yehova,+ chititsani kuti malangizo a Ahitofeli akhale opusa.”+