-
Salimo 88:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kodi chikondi chanu chokhulupirika chingalengezedwe kumanda?
Kodi kukhulupirika kwanu kungalengezedwe mʼmalo a chiwonongeko?*
-
-
Yesaya 38:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Anthu amene akutsikira kudzenje sangayembekezere kuti muwasonyeze kukhulupirika kwanu.+
-