-
Salimo 143:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
143 Inu Yehova, imvani pemphero langa.+
Mvetserani kuchonderera kwanga kopempha thandizo.
Ndiyankheni mogwirizana ndi kukhulupirika kwanu komanso chilungamo chanu.
-