Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 40:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma ine ndine munthu wovutika komanso wosauka.

      Yehova aone zimene zikundichitikira.

      Inu ndi amene mumandithandiza komanso kundipulumutsa.+

      Inu Mulungu wanga, musachedwe.+

  • Salimo 70:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 70 Inu Mulungu, ndipulumutseni,

      Inu Yehova, ndithandizeni mofulumira.+

  • Salimo 71:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mundilanditse ndi kundipulumutsa chifukwa ndinu wolungama.

      Tcherani khutu lanu* kwa ine nʼkundipulumutsa.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani