Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 25:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Inu Mulungu wanga, ndimakudalirani.+

      Musalole kuti ndichite manyazi.+

      Musalole kuti adani anga asangalale chifukwa cha mavuto anga.+

  • Yesaya 50:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Koma Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.+

      Nʼchifukwa chake sindidzamva kuti ndanyozeka.

      Nʼchifukwa chake ndalimbitsa nkhope yanga ngati mwala wa nsangalabwi,+

      Ndipo ndikudziwa kuti sindidzachititsidwa manyazi.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani