-
Yesaya 64:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kuyambira kalekale palibe amene anamvapo, kuganizira,
Kapena kuona Mulungu wina kupatulapo inu,
Amene mumathandiza anthu omwe amayembekezera inu moleza mtima.+
-