1 Samueli 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Sauli anauzidwa kuti: “Davide ali ku Keila.” Ndiyeno Sauli ananena kuti: “Mulungu wamupereka* kwa ine,+ chifukwa wadzitsekereza yekha polowa mumzinda wokhala ndi mageti otsekedwa mwamphamvu.”
7 Kenako Sauli anauzidwa kuti: “Davide ali ku Keila.” Ndiyeno Sauli ananena kuti: “Mulungu wamupereka* kwa ine,+ chifukwa wadzitsekereza yekha polowa mumzinda wokhala ndi mageti otsekedwa mwamphamvu.”