Salimo 148:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutamandeni, inu kumwamba komwe kuli pamwamba kwambiri*Komanso madzi amene ali pamwamba pa kumwamba. 5 Zonsezi zitamande dzina la Yehova,Chifukwa iye analamula ndipo zinalengedwa.+
4 Mutamandeni, inu kumwamba komwe kuli pamwamba kwambiri*Komanso madzi amene ali pamwamba pa kumwamba. 5 Zonsezi zitamande dzina la Yehova,Chifukwa iye analamula ndipo zinalengedwa.+