Salimo 121:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sadzalola kuti phazi lako literereke.*+ Amene akukuyangʼanira sadzawodzera.