Salimo 52:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nʼchifukwa chake Mulungu adzakugwetsa ndipo sudzakhalakonso.+Adzakugwira nʼkukukokera kutali ndi tenti yako,+Ndipo adzakuzula nʼkukuchotsa mʼdziko la anthu amoyo.+ (Selah) 6 Olungama adzaona zimenezi nʼkuchita mantha,+Ndipo adzamuseka+ kuti:
5 Nʼchifukwa chake Mulungu adzakugwetsa ndipo sudzakhalakonso.+Adzakugwira nʼkukukokera kutali ndi tenti yako,+Ndipo adzakuzula nʼkukuchotsa mʼdziko la anthu amoyo.+ (Selah) 6 Olungama adzaona zimenezi nʼkuchita mantha,+Ndipo adzamuseka+ kuti: