Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Yehova adzakhala malo otetezeka* komwe anthu oponderezedwa angathawireko,+

      Malo otetezeka othawirako pa nthawi ya mavuto.+

  • Yesaya 33:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+

      Chiyembekezo chathu chili pa inu.

      Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ mʼmawa uliwonse.

      Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi yamavuto.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani