Yeremiya 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Inu Yehova, ndilangizeni pondipatsa chiweruzo,Koma osati mutakwiya+ chifukwa mungandiwononge.+