Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Levitiko 25:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Musamagulitsiretu malo anu mpaka kalekale+ chifukwa dzikolo ndi langa.+ Kwa ine, inu ndinu alendo mʼdziko langa.+

  • 1 Mbiri 29:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala mʼdziko la eni ngati mmene analili makolo athu onse.+ Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi+ ndipo ndife osakhalitsa.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani