-
Salimo 35:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Koma amene amakonda chilungamo changa afuule mosangalala.
Nthawi zonse azinena kuti:
“Alemekezeke Yehova, amene amasangalala mtumiki wake akakhala pamtendere.”+
-