Salimo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 71:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Adani anga amandinenera zoipa,Ndipo anthu amene akufuna kuchotsa moyo wanga, amandikonzera chiwembu,+11 Iwo akunena kuti: “Mulungu wamusiya. Muthamangitseni nʼkumugwira chifukwa palibe womupulumutsa.”+
10 Adani anga amandinenera zoipa,Ndipo anthu amene akufuna kuchotsa moyo wanga, amandikonzera chiwembu,+11 Iwo akunena kuti: “Mulungu wamusiya. Muthamangitseni nʼkumugwira chifukwa palibe womupulumutsa.”+