-
1 Mbiri 16:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Atamandidwe Yehova Mulungu wa Isiraeli,
Atamandidwe mpaka kalekale.’”
Ndiyeno anthu onse ananena kuti, “Ame!”* ndipo anatamanda Yehova.
-
-
1 Mbiri 29:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako Davide anatamanda Yehova pamaso pa mpingo wonse kuti: “Mutamandidwe inu Yehova Mulungu wa Isiraeli atate wathu, kuyambira kalekale mpaka kalekale.
-