Yesaya 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa tsiku limenelo, mʼdziko la Yuda+ mudzaimbidwa nyimbo+ yakuti: “Ife tili ndi mzinda wolimba.+ Chipulumutso chake chili ngati mipanda yake ndiponso ngati malo ake okwera omenyerapo nkhondo.+
26 Pa tsiku limenelo, mʼdziko la Yuda+ mudzaimbidwa nyimbo+ yakuti: “Ife tili ndi mzinda wolimba.+ Chipulumutso chake chili ngati mipanda yake ndiponso ngati malo ake okwera omenyerapo nkhondo.+