Salimo 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ine ndimakhulupirira inu Yehova.+ Ndipo ndikunena kuti: “Inu ndinu Mulungu wanga.”+