Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mbiri 33:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iye atavutika kwambiri ndi zimenezi, anapempha Yehova kuti amuchitire chifundo* ndipo anadzichepetsa kwambiri pamaso pa Mulungu wa makolo ake. 13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva pemphero lake lochonderera ndiponso lopempha chifundo. Kenako anamʼbwezera ku Yerusalemu ndipo anakhalanso mfumu.+ Zitatero, Manase anadziwa kuti Yehova ndi Mulungu woona.+

  • Salimo 91:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+

      Ndidzakhala naye pa nthawi ya mavuto.+

      Ndidzamupulumutsa komanso kumupatsa ulemerero.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani