Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Nehemiya 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Koma iwo anali osamvera ndipo anakugalukirani.+ Anasiya kutsatira Chilamulo chanu, anapha aneneri anu amene ankawachenjeza kuti abwerere kwa inu ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+

  • Yesaya 5:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Choncho, mofanana ndi mmene lawi la moto limapserezera mapesi

      Komanso mmene udzu wouma umayakira mʼmalawi a moto,

      Mizu yawo idzawola,

      Ndipo maluwa awo adzauluzika ngati fumbi,

      Chifukwa akana malamulo* a Yehova wa magulu ankhondo akumwamba

      Ndipo anyoza mawu a Woyera wa Isiraeli.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani