Salimo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Masoka amene andizungulira ndi ambiri moti sindingathe kuwawerenga.+ Zolakwa zanga ndi zochuluka moti sindikutha kuona kumene ndikulowera.+Zachuluka kwambiri kuposa tsitsi lakumutu kwanga,Ndipo ndataya mtima.
12 Masoka amene andizungulira ndi ambiri moti sindingathe kuwawerenga.+ Zolakwa zanga ndi zochuluka moti sindikutha kuona kumene ndikulowera.+Zachuluka kwambiri kuposa tsitsi lakumutu kwanga,Ndipo ndataya mtima.