Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 4:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mulungu anapatsa Solomo nzeru, luso lozindikira komanso mtima womvetsa zinthu zambirimbiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja.+

  • 1 Mafumu 4:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Anapeka miyambi 3,000+ ndiponso nyimbo zokwana 1,005.+

  • Mlaliki 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kuwonjezera pa kukhala ndi nzeru, wosonkhanitsa anthuyu nthawi zonse ankaphunzitsa anthuwo zimene iye ankadziwa+ ndipo anaganizira mozama komanso anafufuza zinthu mosamala kuti alembe* miyambi yambiri.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani