Miyambo 23:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa hule lili ngati dzenje lakuya,Ndipo mkazi wachiwerewere* ali ngati chitsime chachingʼono.+ 28 Iye amabisalira anthu panjira ngati wachifwamba.+Amachititsa kuti chiwerengero cha amuna osakhulupirika chiwonjezereke.
27 Chifukwa hule lili ngati dzenje lakuya,Ndipo mkazi wachiwerewere* ali ngati chitsime chachingʼono.+ 28 Iye amabisalira anthu panjira ngati wachifwamba.+Amachititsa kuti chiwerengero cha amuna osakhulupirika chiwonjezereke.