Nyimbo ya Solomo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kodi chinthu chikuchokera kuchipululuchi nʼchiyani, chooneka ngati utsi wokwera mʼmwamba,Chonunkhira mafuta a mule ndi lubani,*Komanso ndi zonunkhira zonse za ufa za munthu wamalonda?”+ Nyimbo ya Solomo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nado,+ maluwa a safironi, mabango onunkhira,+ sinamoni,+Komanso mitengo yosiyanasiyana ya lubani, mule, aloye,+Ndi zonunkhira zonse zabwino kwambiri.+
6 “Kodi chinthu chikuchokera kuchipululuchi nʼchiyani, chooneka ngati utsi wokwera mʼmwamba,Chonunkhira mafuta a mule ndi lubani,*Komanso ndi zonunkhira zonse za ufa za munthu wamalonda?”+
14 Nado,+ maluwa a safironi, mabango onunkhira,+ sinamoni,+Komanso mitengo yosiyanasiyana ya lubani, mule, aloye,+Ndi zonunkhira zonse zabwino kwambiri.+