-
Miyambo 15:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Munthu amene amamvetsera chidzudzulo chopatsa moyo,
Amakhala pakati pa anthu anzeru.+
-
-
Miyambo 25:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera+
Amakhala ngati ndolo yagolide ndiponso ngati chokongoletsera chagolide woyenga bwino.
-