Hoseya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Choncho bwerera kwa Mulungu wako.+Uzisonyeza chikondi chokhulupirika ndi chilungamo,+Ndipo nthawi zonse uziyembekezera Mulungu wako.
6 “Choncho bwerera kwa Mulungu wako.+Uzisonyeza chikondi chokhulupirika ndi chilungamo,+Ndipo nthawi zonse uziyembekezera Mulungu wako.