-
1 Mafumu 2:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno Solomo anakhala pampando wachifumu wa Davide bambo ake, ndipo patapita nthawi ufumu wake unakhazikika.+
-
-
2 Mbiri 9:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Solomo analamulira Isiraeli yense ku Yerusalemu kwa zaka 40.
-