Mlaliki 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndinatsimikiza mumtima mwanga kuti ndipeze nzeru ndiponso kuti ndione zinthu zonse* zimene zikuchitika padziko lapansi,+ mpaka kufika pomasala tulo masana ndi usiku.*
16 Ndinatsimikiza mumtima mwanga kuti ndipeze nzeru ndiponso kuti ndione zinthu zonse* zimene zikuchitika padziko lapansi,+ mpaka kufika pomasala tulo masana ndi usiku.*