-
Mlaliki 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu+ ine ndisanakhalepo. Ndipo ndinapitiriza kuchitabe zinthu mwanzeru.
-