-
Nyimbo ya Solomo 8:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Solomo anali ndi munda wa mpesa+ ku Baala-hamoni.
Munda wa mpesawo anaupereka kwa anthu oti aziusamalira.
Ndipo munthu aliyense ankabweretsa ndalama zasiliva zokwana 1,000 zolipirira zipatso za mundawo.
-