-
1 Samueli 8:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Samueli anafotokozera anthu amene ankamupempha kuti awapatse mfumuwo zonse zimene Yehova ananena.
-
-
1 Samueli 8:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ana anu aakazi adzawatenga kuti azikapanga mafuta onunkhira komanso azikaphika mikate ndi zakudya zina.+
-
-
1 Mafumu 9:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma palibe Aisiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo,+ chifukwa iwo anali asilikali ake, atumiki ake, akalonga ake, asilikali othandiza pa magaleta ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta ndi amuna okwera pamahatchi.
-