-
1 Mafumu 4:22, 23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Chakudya cha tsiku lililonse chakunyumba yachifumu ya Solomo chinkakhala ufa wosalala wokwana miyezo 30 ya kori,* ufa wamba wokwana miyezo 60 ya kori, 23 ngʼombe 10 zodyetsera mʼkhola, ngʼombe 20 zodyetsera kutchire, nkhosa 100, mbawala zamphongo, insa, ngondo ndiponso mbalame zoweta.
-