-
Mlaliki 1:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Wosonkhanitsa anthu wanena kuti: “Nʼzachabechabe!
Nʼzachabechabe! Zinthu zonse nʼzachabechabe!”+
-
-
Mlaliki 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,
Ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe, zili ngati kuthamangitsa mphepo.+
-