Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Mlaliki 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndinaona kuti palibe chabwino kuposa kuti munthu asangalale ndi ntchito yake+ chifukwa imeneyo ndi mphoto yake.* Nanga ndi ndani amene angamuchititse kuti aone zimene zidzachitike iye atafa.+

  • Mlaliki 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Mlaliki 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Sangalala ndi moyo limodzi ndi mkazi wako amene umamukonda+ masiku onse a moyo wako wachabechabe, amene Mulungu wakupatsa padziko lapansi pano. Usangalale masiku ako onse achabechabe, chifukwa imeneyi ndi mphoto imene* ukuyenera kulandira pa moyo wako komanso pa ntchito yovuta imene ukuigwira mwakhama padziko lapansi pano.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani