Yobu 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Masiku anga akuthamanga kuposa mashini owombera nsalu,+Atha mofulumira ndipo ine ndilibe chiyembekezo.+ Mlaliki 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa munthu akhoza kugwira ntchito mwakhama ndipo angachite zonse mwanzeru, mozindikira komanso mwaluso. Koma amayenerabe kupereka zonse zimene ali nazo kwa munthu amene sanagwire ntchito iliyonse kuti apeze zinthuzo.+ Zimenezinso nʼzachabechabe ndipo nʼzomvetsa chisoni kwambiri.* Aroma 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
6 Masiku anga akuthamanga kuposa mashini owombera nsalu,+Atha mofulumira ndipo ine ndilibe chiyembekezo.+
21 Chifukwa munthu akhoza kugwira ntchito mwakhama ndipo angachite zonse mwanzeru, mozindikira komanso mwaluso. Koma amayenerabe kupereka zonse zimene ali nazo kwa munthu amene sanagwire ntchito iliyonse kuti apeze zinthuzo.+ Zimenezinso nʼzachabechabe ndipo nʼzomvetsa chisoni kwambiri.*