Miyambo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Manda ndiponso malo achiwonongeko* sakhuta,+Nawonso maso a munthu sakhuta. Mlaliki 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wokonda siliva sakhutira ndi siliva, ndipo wokonda chuma sakhutira ndi phindu limene amapeza.+ Zimenezinso nʼzachabechabe.+
10 Munthu wokonda siliva sakhutira ndi siliva, ndipo wokonda chuma sakhutira ndi phindu limene amapeza.+ Zimenezinso nʼzachabechabe.+