-
Yesaya 40:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Tamvera! Winawake akunena kuti: “Lengeza mofuula!”
Wina akufunsa kuti: “Ndilengeze mofuula za chiyani?”
“Anthu onse ali ngati udzu wobiriwira.
Chikondi chawo chonse chokhulupirika chili ngati duwa lakutchire.+
-