- 
	                        
            
            Nyimbo ya Solomo 4:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        4 “Ndiwe wokongola wokondedwa wanga. Ndiwe chiphadzuwa. Maso ako ali ngati maso a njiwa munsalu yako yophimba kumutuyo. Tsitsi lako lili ngati gulu la mbuzi Zimene zikuthamanga potsika mapiri a ku Giliyadi.+ 
 
-