- 
	                        
            
            Nyimbo ya Solomo 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        9 Wachikondi wanga ali ngati insa komanso mphoyo yaingʼono.+ Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma la nyumba yathu. Akuyangʼana mʼmawindo, Akusuzumira pazotchingira mʼmawindo. 
 
- 
                                        
- 
	                        
            
            Nyimbo ya Solomo 8:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        14 “Fulumira wachikondi wanga, Thamanga ngati insa+ Kapena ngati mphoyo yaingʼono Pamapiri amaluwa onunkhira.” 
 
-