-
Nyimbo ya Solomo 5:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndinamʼtsegulira wachikondi wanga,
Koma wachikondi wangayo anali atachokapo, atapita.
Ndinadandaula kwambiri atachoka.
Ndinamufunafuna koma sindinamupeze.+
Ndinamuitana koma sanandiyankhe.
-