-
Nyimbo ya Solomo 5:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Alonda amene ankazungulira mumzinda anandipeza.
Anandimenya ndipo anandivulaza.
Alonda apamipanda anandilanda chofunda changa.*
-