2 Samueli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Davide anatonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kenako anagona naye ndipo patapita nthawi, anabereka mwana wamwamuna yemwe anamupatsa dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anamʼkonda mwana ameneyu,+ Miyambo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
24 Ndiyeno Davide anatonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kenako anagona naye ndipo patapita nthawi, anabereka mwana wamwamuna yemwe anamupatsa dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anamʼkonda mwana ameneyu,+